Yoswa 21:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Kuchokera ku hafu ya fuko la Manase, anawapatsa Taanaki+ ndi malo ake odyetserako ziweto ndiponso Gati-rimoni ndi malo ake odyetserako ziweto. Inalipo mizinda iwiri.
25 Kuchokera ku hafu ya fuko la Manase, anawapatsa Taanaki+ ndi malo ake odyetserako ziweto ndiponso Gati-rimoni ndi malo ake odyetserako ziweto. Inalipo mizinda iwiri.