Yoswa 22:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Simunawasiye abale anu nthawi yonseyi mpaka lero+ ndipo mwasunga malamulo a Yehova Mulungu wanu.+