Yoswa 22:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kenako Aisiraeli ena anamva+ anthu akunena kuti: “Eti anthu a fuko la Rubeni, la Gadi ndi hafu ya fuko la Manase amanga guwa lansembe mʼmalire a dziko la Kanani, mʼchigawo cha Yorodano kumbali ya Aisiraeli.”
11 Kenako Aisiraeli ena anamva+ anthu akunena kuti: “Eti anthu a fuko la Rubeni, la Gadi ndi hafu ya fuko la Manase amanga guwa lansembe mʼmalire a dziko la Kanani, mʼchigawo cha Yorodano kumbali ya Aisiraeli.”