Yoswa 22:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Anthu onse a Yehova anena kuti: ‘Nʼchifukwa chiyani mwachita zosakhulupirika+ kwa Mulungu wa Isiraeli? Lero mwasiya kutsatira Yehova pomanga guwa lanu lansembe kuti mupandukire Yehova.+
16 “Anthu onse a Yehova anena kuti: ‘Nʼchifukwa chiyani mwachita zosakhulupirika+ kwa Mulungu wa Isiraeli? Lero mwasiya kutsatira Yehova pomanga guwa lanu lansembe kuti mupandukire Yehova.+