-
Yoswa 22:19Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
19 Ngati chili chifukwa choti dziko lanu ndi lodetsedwa, wolokerani kudziko la Yehova+ kumene kuli tenti yopatulika ya Yehova*+ ndipo muzikakhala nafe. Koma musapandukire Yehova, ndipo musachititse ifeyo kupanduka chifukwa cha guwa lansembe limene mwamangali, kuwonjezera pa guwa lansembe la Yehova Mulungu wathu.+
-