Yoswa 22:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ngati tadzimangira guwa lansembe kuti tisiye kutsatira Yehova ndiponso ngati timafuna kuti tiziperekerapo nsembe zopsereza ndi nsembe zambewu komanso nsembe zachiyanjano, Yehova apereka yekha chilango.+
23 Ngati tadzimangira guwa lansembe kuti tisiye kutsatira Yehova ndiponso ngati timafuna kuti tiziperekerapo nsembe zopsereza ndi nsembe zambewu komanso nsembe zachiyanjano, Yehova apereka yekha chilango.+