27 koma kuti ukhale umboni pakati pa ife ndi inu+ komanso ana athu, wakuti tidzatumikira Yehova ndi nsembe zathu zopsereza, nsembe zachiyanjano ndi nsembe zina,+ kuti mʼtsogolo ana anu asadzauze ana athu kuti: “Inuyo zolambira Yehova sizikukukhudzani.”’