-
Yoswa 22:28Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
28 Choncho tinati, ‘Akadzatiuza zimenezi ifeyo kapena ana athu mʼtsogolo, tidzawauza kuti: “Onani guwa lansembe limene makolo athu anamanga lofanana ndi guwa la Yehova, osati kuti aziperekerapo nsembe zopsereza kapena nsembe zina, koma kuti likhale umboni pakati pa inu ndi ife.”’
-