-
Yoswa 22:32Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
32 Kenako Pinihasi mwana wa wansembe Eliezara ndi atsogoleri aja, anachoka kwa anthu a fuko la Rubeni ndi la Gadi ku Giliyadi, nʼkubwerera kwa Aisiraeli ena ku Kanani. Ndipo anawafotokozera zimene anthu a fuko la Rubeni ndi la Gadi ananena.
-