Yoswa 22:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Choncho anthu a fuko la Rubeni ndi la Gadi analitcha dzina guwalo,* chifukwa anati, “Guwali ndi mboni pakati pathu kuti Yehova ndi Mulungu woona.” Yoswa Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 22:34 Nsanja ya Olonda,11/1/1986, tsa. 22
34 Choncho anthu a fuko la Rubeni ndi la Gadi analitcha dzina guwalo,* chifukwa anati, “Guwali ndi mboni pakati pathu kuti Yehova ndi Mulungu woona.”