Yoswa 23:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Inuyo mwaona zonse zimene Yehova Mulungu wanu anachitira mitundu yonseyi chifukwa cha inu. Yehova Mulungu wanu ndi amene ankakumenyerani nkhondo.+
3 Inuyo mwaona zonse zimene Yehova Mulungu wanu anachitira mitundu yonseyi chifukwa cha inu. Yehova Mulungu wanu ndi amene ankakumenyerani nkhondo.+