Yoswa 23:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Yehova adzathamangitsa mitundu ikuluikulu ndiponso yamphamvu kuichotsa kwa inu+ chifukwa mpaka pano, palibe munthu ndi mmodzi yemwe amene wakwanitsa kulimbana nanu.+
9 Yehova adzathamangitsa mitundu ikuluikulu ndiponso yamphamvu kuichotsa kwa inu+ chifukwa mpaka pano, palibe munthu ndi mmodzi yemwe amene wakwanitsa kulimbana nanu.+