Yoswa 23:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma mofanana ndi malonjezo onse abwino amene Yehova Mulungu wanu ananena omwe akwaniritsidwa pa inu,+ Yehova adzakwaniritsanso pa inu masoka onse* amene ananena, ndipo adzakufafanizani padziko labwino limene Yehova Mulungu wanu wakupatsanili.+
15 Koma mofanana ndi malonjezo onse abwino amene Yehova Mulungu wanu ananena omwe akwaniritsidwa pa inu,+ Yehova adzakwaniritsanso pa inu masoka onse* amene ananena, ndipo adzakufafanizani padziko labwino limene Yehova Mulungu wanu wakupatsanili.+