Yoswa 24:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Patapita nthawi, ndinatenga kholo lanu Abulahamu+ kuchokera kutsidya lina la Mtsinje.* Ndinamuyendetsa mʼdziko lonse la Kanani ndipo ndinachulukitsa mbadwa zake.*+ Ndinamʼpatsa Isaki+ Yoswa Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 24:3 Nsanja ya Olonda,8/15/2001, tsa. 14
3 Patapita nthawi, ndinatenga kholo lanu Abulahamu+ kuchokera kutsidya lina la Mtsinje.* Ndinamuyendetsa mʼdziko lonse la Kanani ndipo ndinachulukitsa mbadwa zake.*+ Ndinamʼpatsa Isaki+