Oweruza 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndiyeno Yuda anauza mʼbale wake Simiyoni kuti: “Tiye tipitire limodzi mʼgawo langa+ kuti tikamenyane ndi Akanani. Kenako inenso ndidzapita nawe kugawo lako.” Choncho Simiyoni anapita naye.
3 Ndiyeno Yuda anauza mʼbale wake Simiyoni kuti: “Tiye tipitire limodzi mʼgawo langa+ kuti tikamenyane ndi Akanani. Kenako inenso ndidzapita nawe kugawo lako.” Choncho Simiyoni anapita naye.