Oweruza 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Anapeza Adoni-bezeki ku Bezeki nʼkumenyana naye ndipo anagonjetsa Akanani+ ndi Aperezi.+