Oweruza 1:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kenako Kalebe+ anati: “Aliyense amene agonjetse mzinda wa Kiriyati-seferi nʼkuulanda, ndidzamʼpatsa mwana wanga Akisa, kuti akhale mkazi wake.”+
12 Kenako Kalebe+ anati: “Aliyense amene agonjetse mzinda wa Kiriyati-seferi nʼkuulanda, ndidzamʼpatsa mwana wanga Akisa, kuti akhale mkazi wake.”+