Oweruza 1:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pamene Akisa ankapita kunyumba, anauza Otiniyeli kuti apemphe munda kwa Kalebe bambo ake. Kenako Akisa anatsika pabulu.* Atatero, Kalebe anamufunsa kuti: “Ukufuna chiyani?”
14 Pamene Akisa ankapita kunyumba, anauza Otiniyeli kuti apemphe munda kwa Kalebe bambo ake. Kenako Akisa anatsika pabulu.* Atatero, Kalebe anamufunsa kuti: “Ukufuna chiyani?”