-
Oweruza 1:26Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
26 Ndiyeno mwamunayo anapita kudziko la Ahiti ndi kumanga mzinda ndipo anaupatsa dzina loti Luzi. Limeneli ndi dzina la mzindawo mpaka lero.
-