Oweruza 1:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Fuko la Zebuloni silinathamangitse anthu okhala mumzinda wa Kitironi ndi mzinda wa Nahaloli,+ moti Akananiwo anapitiriza kukhala pakati pawo ndipo a fuko la Zebuloni anayamba kugwiritsa ntchito yaukapolo Akananiwo.+
30 Fuko la Zebuloni silinathamangitse anthu okhala mumzinda wa Kitironi ndi mzinda wa Nahaloli,+ moti Akananiwo anapitiriza kukhala pakati pawo ndipo a fuko la Zebuloni anayamba kugwiritsa ntchito yaukapolo Akananiwo.+