Oweruza 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Yoswa atauza Aisiraeliwo kuti azipita, aliyense anapita komwe kunali cholowa chake, kukatenga dzikolo kukhala lawo.+
6 Yoswa atauza Aisiraeliwo kuti azipita, aliyense anapita komwe kunali cholowa chake, kukatenga dzikolo kukhala lawo.+