Oweruza 2:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Anthuwo anapitiriza kutumikira Yehova masiku onse amene Yoswa anali ndi moyo komanso masiku onse a akulu amene anakhalabe ndi moyo Yoswa atamwalira, omwe anaona zinthu zazikulu zimene Yehova anachitira Aisiraeli.+
7 Anthuwo anapitiriza kutumikira Yehova masiku onse amene Yoswa anali ndi moyo komanso masiku onse a akulu amene anakhalabe ndi moyo Yoswa atamwalira, omwe anaona zinthu zazikulu zimene Yehova anachitira Aisiraeli.+