Oweruza 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Iwo anasiya Yehova, Mulungu wa makolo awo amene anawatulutsa mʼdziko la Iguputo+ nʼkuyamba kutsatira milungu ya anthu owazungulira.+ Anayamba kugwadira milunguyo ndipo anakhumudwitsa Yehova.+
12 Iwo anasiya Yehova, Mulungu wa makolo awo amene anawatulutsa mʼdziko la Iguputo+ nʼkuyamba kutsatira milungu ya anthu owazungulira.+ Anayamba kugwadira milunguyo ndipo anakhumudwitsa Yehova.+