Oweruza 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Zikatero, Yehova ankawapatsa oweruza omwe ankawapulumutsa mʼmanja mwa adani.+