Oweruza 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Yehova analola mitundu yotsatirayi kukhalabe mʼdzikoli nʼcholinga choti ayese Aisiraeli onse amene anali asanaonepo nkhondo zimene mtunduwo unamenya ku Kanani.+
3 Yehova analola mitundu yotsatirayi kukhalabe mʼdzikoli nʼcholinga choti ayese Aisiraeli onse amene anali asanaonepo nkhondo zimene mtunduwo unamenya ku Kanani.+