Oweruza 3:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Aisiraeli ankakwatira ana aakazi a Akanani ndipo ana awo aakazi ankawapereka kwa ana aamuna a Akananiwo, ndipo Aisiraeli anayamba kulambira milungu ya Akanani.+
6 Aisiraeli ankakwatira ana aakazi a Akanani ndipo ana awo aakazi ankawapereka kwa ana aamuna a Akananiwo, ndipo Aisiraeli anayamba kulambira milungu ya Akanani.+