Oweruza 3:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ehudi anali atapanga lupanga lakuthwa konsekonse, lotalika mkono umodzi,* ndipo analimangirira mʼchiuno kumanja, mkati mwa chovala chake. Oweruza Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 3:16 Nsanja ya Olonda,3/15/2004, tsa. 303/15/1997, ptsa. 29-30
16 Ehudi anali atapanga lupanga lakuthwa konsekonse, lotalika mkono umodzi,* ndipo analimangirira mʼchiuno kumanja, mkati mwa chovala chake.