-
Oweruza 3:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Ehudi atapereka msonkhowo, iye ndi anthu amene ananyamula msonkhowo ananyamuka nʼkumapita.