19 Koma atafika pamafano osema amene anali ku Giligala,+ anabwerera kwa mfumu nʼkunena kuti: “Pepanitu mfumu, ndili ndi uthenga wachinsinsi woti ndikuuzeni.” Choncho mfumuyo inati: “Tipatseni mpata!” Itanena zimenezi, atumiki onse a mfumuyo anatuluka.