-
Oweruza 3:21Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
21 Ndiyeno Ehudi, pogwiritsa ntchito dzanja lamanzere, anasolola lupanga lomwe linali mʼchiuno mwake kumanja nʼkubaya nalo Egiloni mʼmimba.
-