-
Oweruza 3:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Lupangalo linalowa ndi chogwirira chomwe ndipo mafuta anaphimba lupangalo chifukwa sanalizule mʼmimba mwakemo, ndipo chimbudzi chinayamba kutuluka.
-