-
Oweruza 3:25Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
25 Iwo anadikira mpaka kutaya mtima chifukwa anaona kuti mfumu sikutsegula zitseko za chipinda chapadenga. Choncho anatenga kiyi nʼkutsegula zitsekozo ndipo anangoona mbuye wawo ali kwala pansi, atafa.
-