Oweruza 3:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Pa nthawi imeneyo anapha Amowabu pafupifupi 10,000.+ Onse anali asilikali amphamvu komanso olimba mtima, koma panalibe ngakhale mmodzi amene anapulumuka.+
29 Pa nthawi imeneyo anapha Amowabu pafupifupi 10,000.+ Onse anali asilikali amphamvu komanso olimba mtima, koma panalibe ngakhale mmodzi amene anapulumuka.+