Oweruza 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Debora anatumiza uthenga kwa Baraki+ mwana wa Abinowamu, yemwe anali ku Kedesi-nafitali,+ womuuza kuti: “Yehova Mulungu wa Isiraeli walamula kuti, ‘Tenga amuna 10,000 a fuko la Nafitali ndi la Zebuloni ndipo mukasonkhane paphiri la Tabori. Oweruza Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:6 Nsanja ya Olonda,11/15/2003, ptsa. 28-29
6 Debora anatumiza uthenga kwa Baraki+ mwana wa Abinowamu, yemwe anali ku Kedesi-nafitali,+ womuuza kuti: “Yehova Mulungu wa Isiraeli walamula kuti, ‘Tenga amuna 10,000 a fuko la Nafitali ndi la Zebuloni ndipo mukasonkhane paphiri la Tabori.