-
Oweruza 4:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Ndiyeno Baraki anauza Debora kuti: “Ngati ungapite nane, ndipita, koma ngati supita nane, sindipita.”