-
Oweruza 4:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Kenako Debora anauza Baraki kuti: “Nyamuka, chifukwa lero ndi limene Yehova apereke Sisera mʼmanja mwako. Yehova akuyendatu patsogolo pako.” Baraki anatsikadi mʼphiri la Tabori, amuna 10,000 akumʼtsatira.
-