Oweruza 4:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Koma Sisera anathawa wapansi kupita kutenti ya Yaeli,+ mkazi wa Hiberi+ Mkeni, chifukwa panali mtendere pakati pa Yabini+ mfumu ya Hazori ndi banja la Hiberi Mkeni. Oweruza Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 4:17 Nsanja ya Olonda,8/1/2015, tsa. 14
17 Koma Sisera anathawa wapansi kupita kutenti ya Yaeli,+ mkazi wa Hiberi+ Mkeni, chifukwa panali mtendere pakati pa Yabini+ mfumu ya Hazori ndi banja la Hiberi Mkeni.