-
Oweruza 4:18Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
18 Ndiyeno Yaeli anatuluka kukachingamira Sisera nʼkumuuza kuti: “Fikani mbuyanga, lowani. Musaope.” Choncho anapita nʼkukalowa mutenti ya Yaeli ndipo anamʼfunditsa bulangete.
-