Oweruza 4:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kenako Sisera anamuuza kuti: “Ndipatse madzi akumwa, chifukwa ndili ndi ludzu.” Choncho anatsegula thumba lachikopa la mkaka ndi kumʼpatsa kuti amwe.+ Atatero, anamʼfunditsanso.
19 Kenako Sisera anamuuza kuti: “Ndipatse madzi akumwa, chifukwa ndili ndi ludzu.” Choncho anatsegula thumba lachikopa la mkaka ndi kumʼpatsa kuti amwe.+ Atatero, anamʼfunditsanso.