-
Oweruza 4:20Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
20 Sisera anauza Yaeli kuti: “Uime pakhomo la tenti, ndipo pakabwera munthu nʼkukufunsa kuti, ‘Kodi pali mwamuna aliyense pano?’ umuuze kuti, ‘Palibe.’”
-