-
Oweruza 4:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Zitatero Baraki anatulukira akusakasaka Sisera. Kenako Yaeli anapita kukamuchingamira, ndipo anamuuza kuti: “Bwerani ndikuonetseni munthu amene mukumʼfunafunayo.” Iye anamʼtsatira ndipo anangoona Sisera ali kwala atafa, mʼmutu mwake muli chikhomo pafupi ndi khutu.
-