Oweruza 4:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Choncho pa tsikuli Mulungu anagonjetsa Yabini mfumu ya Kanani, pamaso pa Aisiraeli.+