Oweruza 4:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndipo dzanja la Aisiraeli linapitiriza kukula mphamvu pomenyana ndi Yabini mfumu ya Kanani,+ mpaka anapha Yabini mfumu ya Kanani.+
24 Ndipo dzanja la Aisiraeli linapitiriza kukula mphamvu pomenyana ndi Yabini mfumu ya Kanani,+ mpaka anapha Yabini mfumu ya Kanani.+