Oweruza 5:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Anthu a ku Giliyadi anangokhala kutsidya lina la Yorodano.+Ndipo nʼchifukwa chiyani Dani anangokhala mʼsitima?*+ Aseri anangokhala phee mʼmbali mwa nyanja,Osachoka pamadoko ake.+
17 Anthu a ku Giliyadi anangokhala kutsidya lina la Yorodano.+Ndipo nʼchifukwa chiyani Dani anangokhala mʼsitima?*+ Aseri anangokhala phee mʼmbali mwa nyanja,Osachoka pamadoko ake.+