Oweruza 6:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Aisiraeli akalima minda yawo, Amidiyani, Aamaleki+ ndi anthu a Kumʼmawa+ ankabwera kudzawaukira.