-
Oweruza 6:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 Kenako iye anati: “Ngati mwandikomera mtima, mundionetse chizindikiro kuti nditsimikize kuti ndinudi amene mukulankhula nane.
-