Oweruza 6:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Kenako mngelo wa Yehova anakhudza nyama ndi mikateyo ndi nsonga ya ndodo imene inali mʼmanja mwake. Atatero, moto unayaka pamwalawo nʼkuwotcheratu nyama ndi mkatewo.+ Zitatero mngelo wa Yehovayo anazimiririka.
21 Kenako mngelo wa Yehova anakhudza nyama ndi mikateyo ndi nsonga ya ndodo imene inali mʼmanja mwake. Atatero, moto unayaka pamwalawo nʼkuwotcheratu nyama ndi mkatewo.+ Zitatero mngelo wa Yehovayo anazimiririka.