Oweruza 6:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Umangire Yehova Mulungu wako guwa lansembe poyala miyala pamwamba pa malo otetezekawa. Ukatero, utenge ngʼombe yaingʼono yamphongo yachiwiri ija nʼkuipereka monga nsembe yopsereza pankhuni za mzati wopatulika* umene udulewo.”
26 Umangire Yehova Mulungu wako guwa lansembe poyala miyala pamwamba pa malo otetezekawa. Ukatero, utenge ngʼombe yaingʼono yamphongo yachiwiri ija nʼkuipereka monga nsembe yopsereza pankhuni za mzati wopatulika* umene udulewo.”