Oweruza 6:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Amidiyani+ ndi Aamaleki onse,+ pamodzi ndi anthu onse a Kumʼmawa anasonkhanitsa asilikali awo+ ndipo anawoloka mtsinje nʼkukamanga msasa mʼchigwa cha Yezereeli. Oweruza Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 6:33 Nsanja ya Olonda,2/15/1986, ptsa. 21-22
33 Amidiyani+ ndi Aamaleki onse,+ pamodzi ndi anthu onse a Kumʼmawa anasonkhanitsa asilikali awo+ ndipo anawoloka mtsinje nʼkukamanga msasa mʼchigwa cha Yezereeli.