-
Oweruza 7:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Komabe, Yehova anauza Gidiyoni kuti: “Anthu amene atsalawa adakali ambiri. Pita nawo kumadzi kuti ndikawayese kumeneko. Amene ndikakuuze kuti, ‘Uyu apite nawe,’ ukapite naye, koma amene ndikakuuze kuti, ‘Uyu asapite,’ usakapite naye.”
-